- Uncategorized
MAFUNSO OKHUDZA KUKHULUPIRIRA MWA ALLAH
MAFUNSO OKHUDZA KUKHULUPIRIRA MWA ALLAH Ndithu mafunso omwe amakonda kuzungulira kwambiri mmutu wa mwana akakhala wachichepere kwambiri ndiwo mafunsa okhudza…
Read More » MAU OYAMBA
Ndithu kutamandidwa konse ndi kwa Allah bwana wazolengwedwa zonse, ndipo madalitso ndi mtendere zipite kwa wolemekezeka wa aneneri onse wa…
Read More »- topicsSw
ZOKHUDZA MAPHUNZIRO A za CHIKHULUPILIRO
Ndithu maphunziro ndi chimozi mwazinthu zofunikira kwambiri pokhonza munthu, ndipo ndi chipangizo chokonzera mwana ndi kumpatsira maziko ambali zonse za…
Read More » - topicsSw
MAPHUNZIRO A ZA CHIKHULUPILIRO A ANA
Maphunziro azachikhulupiliro pa ana ndi umodzi mwamitu yofunikira kwambiri pamaphunziro potengera zimene zikupezeka mkati mwa maphunziro, chifukwa ndi umene umakhazikitsa…
Read More » - topicsSw